Download Namadingo – Sakaka Mp3 & Lyrics
uvomereze mbali yako wachita
kodi uchite kudzichekacheka
kut amvetsetse usachite kumuumiliza kut mukondane
kodi udzimupembedza kut akukonde usachite kuyaluka nazo
(chorus)
chikondi sakaka kakamizana
chikondi sitikakamila
ngt watopa mulekele
mulekeleo
ngt walema muchokere
osakakamizana
abwere ndi nzeru zake
the mind the body the soul
adzikukonda iwe udzidziwaso
udzichita kumva kut wina palibeso
zija zomalotana mukatseka maso
she be the king nah iwe the king in a castel
not zija zombetsana kuwawaso
Quotable Lyrics
Download Namadingo Chikondi Sakakamizana mp3
Download Chikondi Sakaka – Namadingo Sakaka mizana Audio Download